1Adamu, Seti, Enosi
2Kenani, Mahalaleli, Yaredi,
3Enoki, Metusela, Lameki, Nowa.
4Ana a Nowa, Semu, Hamu ndi Yafeti.
5Ana aamuna a Yafeti anali:
5Gomeri, Magogi, Madai, Yavani, Tubala, Mesaki ndi Tirasi.
6Ana aamuna a Gomeri anali:
6Asikenazi, Rifati ndi Togarima
7Ana aamuna a Yavani anali:
7Elisa, Tarisisi, Kitimu ndi Rodanimu.
8Ana aamuna a Hamu anali:
8Kusi, Miziraimu, Puti ndi Kanaani
9Ana aamuna a Kusi anali: Ana aamuna a Raama anali: Seba ndi Dedani.
9Seba, Havila, Sabita, Raama ndi Sabiteka
10Kusi anali abambo a Nimurodi amene anali wankhondo wamphamvu
10kwambiri pa dziko lapansi.
11Igupto ndiye kholo la
11Aludi, Aanami, Alehabu, Anafutu,
12Apaturusi, Akasilu (kumene kunachokera Afilisti) ndi Akafitori.
12
13Kanaani anabereka mwana wake wachisamba Sidoni,
13ndipo anaberekanso Ahiti,
14Ayebusi, Aamori, Agirigasi
15Ahivi, Aariki, Asini
16Aaravadi, Azemari ndi Ahamati.
16
17Ana aamuna a Semu anali: Ana aamuna a Aramu anali: Uzi, Huri, Geteri ndi Mesaki.
17Elamu, Asuri, Aripakisadi, Ludi ndi Aramu.
18Aripakisadi anabereka Sela
18ndipo Selayo anabereka Eberi:
19Eberi anabereka ana aamuna awiri:
19wina anamutcha Pelegi, chifukwa pa nthawiyo anthu a pa dziko lapansi anagawikana. Dzina la mʼbale wake linali Yokitani.
20Yokitani anabereka
20Alimodadi, Selefi, Hazari-Maveti, Yera,
21Hadoramu, Uzali, Dikila
22Obali, Abimaeli, Seba,
23Ofiri, Havila ndi Yobabu. Onsewa anali ana aamuna a Yokitani.
23
24Semu, Aripakisadi, Sela
26
27ndi Abramu (amene ndi Abrahamu).
27
28Ana a Abrahamu ndi awa:
28Isake ndi Ismaeli.
29Zidzukulu zake zinali izi:
29Nebayoti ndiye anali mwana woyamba wa Ismaeli, kenaka Kedara, Adibeeli, Mibisamu,
30Misima, Duma, Masa, Hadadi, Tema,
31Yeturi, Nafisi ndi Kedema. Awa anali ana a Ismaeli.
31
32Ana a Ketura mzikazi wa Abrahamu anali awa: Ana a Yokisani ndi awa: Seba ndi Dedani
32Zimurani, Yokisani, Medani, Midiyani, Isibaki ndi Suwa.
33Ana aamuna a Midiyani anali, Onsewa anali zidzukulu za Ketura.
33Efai, Eferi, Hanoki, Abida ndi Elida.
34Abrahamu anabereka Isake. Esau ndi Israeli.
34Ana a Isake anali awa:
35Ana aamuna a Esau anali awa:
35Elifazi, Reueli, Yeusi, Yolamu ndi Kora.
36Ana a Elifazi anali awa: Amene anabereka ndi Timna: Amaleki.
36Temani, Omari, Zefo, Gatamu ndi Kenazi:
37Ana a Reueli anali awa:
37Nahati, Zera, Sama ndi Miza.
38Ana a Seiri anali awa:
38Lotani, Sobala, Zibeoni, Ana, Disoni, Ezeri ndi Disani.
39Ana aamuna a Lotani anali awa:
39Hori ndi Homamu. Timna anali mlongo wake wa Lotani.
40Ana aamuna a Sobala anali awa: Ana aamuna a Zibeoni anali awa: Ayiwa ndi Ana.
40Alivani, Manahati, Ebala, Sefo ndi Onamu.
41Mwana wa Ana anali Ana a Disoni anali awa: Hemudani, Esibani, Itirani ndi Kerani
41Disoni.
42Ana aamuna a Ezeri anali awa: Ana aamuna a Disani anali awa: Uzi ndi Arani.
42Bilihani, Zaavani ndi Yaakani.
43Awa ndi mafumu amene ankalamulira dziko la Edomu, mfumu iliyonse ya Israeli isanayambe kulamulira kumeneko:
43Bela mwana wa Beori, mzinda wake ankawutcha Dinihaba.
44Bela atamwalira, Yobabu mwana wa Zera wochokera ku Bozira analowa ufumu mʼmalo mwake.
44
45Yobabu atamwalira, Husamu wochokera ku dziko la Atemani, analowa ufumu mʼmalo mwake.
45
46Husamu atamwalira, Hadadi mwana wa Bedadi, amene anagonjetsa Amidiyani mʼdziko la Mowabu, analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Aviti.
46
47Hadadi atamwalira, Samila wochokera ku Masireka analowa ufumu mʼmalo mwake.
47
48Samila atamwalira, Sauli wochokera ku Rehoboti wa ku Mtsinje analowa ufumu mʼmalo mwake.
48
49Sauli atamwalira, Baala-Hanani mwana wa Akibori analowa ufumu mʼmalo mwake.
49
50Pamene Baala-Hanani anamwalira, Hadadi analowa ufumu mʼmalo mwake. Mzinda wake unkatchedwa Pau, ndipo dzina la mkazi wake linali Mehatabeli mwana wa Matiredi, mwana wamkazi wa Me-Zahabu.
51Hadadi anamwaliranso. Timna, Aliva, Yeteti,
51Mafumu a ku Edomu anali:
52Oholibama, Ela, Pinoni,
53Kenazi, Temani, Mibezari,
54Magidieli ndi Iramu. Awa anali mafumu a ku Edomu.