1 Ana aamuna a Davide amene anabadwira ku Hebroni anali awa: Woyamba anali Amnoni, amayi ake anali Ahinoamu wa ku Yezireeli; wachiwiri anali Danieli, amayi ake anali Abigayeli wa ku Karimeli;
2 wachitatu anali Abisalomu, mwana wa Maaka mwana wa Talimai mfumu ya Gesuri;
2 wachinayi anali Adoniya amayi ake anali Hagiti;
3 wachisanu anali Sefatiya, amayi ake anali Abitali;
3 wachisanu ndi chimodzi anali Itireamu, amayi ake anali Egila.
4 Ana asanu ndi mmodzi awa a Davide anabadwira ku Hebroni kumene analamulirako zaka zisanu ndi ziwiri ndi miyezi isanu ndi umodzi.
4 Davide analamuliranso mu Yerusalemu kwa zaka 33,
5 ndipo ana amene anabadwira ku Yerusalemuko anali awa:
5 Samua, Sobabu, Natani ndi Solomoni. Ana anayi awa anali a Batisuwa mwana wa Amieli.
6 Anaberekanso Ibihari, Elisua, Elipeleti,
7 Noga, Nefegi, Yafiya,
8 Elisama, Eliada ndi Elifeleti, onse analipo asanu ndi anayi.
9 Onsewa anali ana a Davide, osawerengera ana a azikazi. Ndipo mlongo wawo anali Tamara.
9
10 Mwana wa Solomoni anali Rehabiamu, Abiya anabereka Asa, Asa anabereka Yehosafati,
10 Rehabiamu anabereka Abiya,
11 Yehosafati anabereka Yehoramu, Ahaziya anabereka Yowasi,
11 Yehoramu anabereka Ahaziya,
12 Yowasi anabereka Amaziya, Azariya anabereka Yotamu,
12 Amaziya anabereka Azariya,
13 Yotamu anabereka Ahazi, Hezekiya anabereka Manase,
13 Ahazi anabereka Hezekiya,
14 Manase anabereka Amoni,
14 Amoni anabereka Yosiya.
15 Ana a Yosiya anali awa: Yehoyakimu mwana wake wachiwiri, Zedekiya mwana wake wachitatu, Salumu mwana wake wachinayi.
15 Yohanani mwana wake woyamba,
16 Ana a Yehoyakimu: ndi Zedekiya mwana wake.
16 Yekoniya
17 Zidzukulu za Yekoniya wa mʼndende zinali izi:
17 mwana wake Silatieli,
18 Malikiramu, Pedaya, Senazara, Yekamiya, Hosama ndi Nedabiya.
18
19 Ana a Pedaya anali awa: Ana a Zerubabeli anali awa: Mesulamu ndi Hananiya. Mlongo wawo anali Selomiti.
19 Zerubabeli ndi Simei.
20 Panalinso ana ena asanu awa:
20 Hasubu, Oheli, Berekiya, Hasabiya ndi Yusabu-Hesedi.
21 Zidzukulu za Hananiya zinali izi:
21 Pelatiya ndi Yesaiya, ndiponso ana a Refaya, ana a Arinani, ana a Obadiya ndi ana a Sekaniya.
22 Zidzukulu za Sekaniya zinali izi: Hatusi, Igala, Bariya, Neariya ndi Safati. Onse anali asanu ndi mmodzi.
22 Semaya ndi ana ake:
23 Ana a Neariya anali awa:
23 Eliyoenai, Hezekiya ndi Azirikamu. Onse anali atatu.
24 Ana a Eliyoenai: Hodaviya, Eliyasibu, Pelaya, Akubu,
24 Yohanani, Delaya ndi Anani, onse anali asanu ndi awiri.
Copyright © 2002, 2016 by Biblica, Inc.® Used by permission of Biblica, Inc.® All rights reserved worldwide. Mwini © 2002, 2016 ndi Biblica, Inc.® Kugwiritsa ntchito mwachilolezo. Umwini ndi otetezedwa pa dziko lonse.