15Ana a Kalebe mwana wa Yefune anali awa: Mwana wa Ela anali Kenazi.
15Iru, Ela ndi Naama.
16Ana a Yehaleleli anali awa:
16Zifi, Zifa, Tiriya ndi Asareli.
17Ana a Ezara anali awa:
17Yeteri, Meredi, Eferi ndi Yaloni. Mmodzi mwa akazi a Meredi anabereka Miriamu, Samai ndi Isiba abambo ake a Esitemowa.
18(Mkazi wake wa Chiyuda anabereka Yaredi abambo ake a Gedori, Heberi abambo ake a Soko ndi Yekutieli abambo a Zanowa). Awa anali ana a mwana wamkazi wa Farao, Bitia, amene Meredi anakwatira.
18
19Ana a mkazi wa Hodiya, mlongo wa Nahamu anali awa:
19abambo ake a Keila wa ku Garimi ndi Esitemowa wa ku Maaka.
20Ana a Simeoni anali awa: Ana a Isi anali awa: Zoheti ndi Beni-Zoheti.
20Amnoni, Rina, Beni-Hanani ndi Tiloni.
21Ana a Sela mwana wa Yuda anali awa:
21Eri amene anabereka Leka, Laada amene anabereka Maresa ndi mabanja a anthu owomba nsalu zofewa ndi zosalala a ku Beti-Asibeya,
22Yokimu, anthu a ku Kozeba, ndiponso Yowasi ndi Sarafi, amene ankalamulira Mowabu ndi Yasibu-Lehemu. (Nkhani zimenezi ndi zakalekale).
23Iwo anali owumba mbiya amene ankakhala ku Netaimu ndi Gederi. Ankakhala kumeneko ndi kumatumikira mfumu.
23
24Ana a Simeoni anali awa:
24Nemueli, Yamini, Yaribu, Zera ndi Sauli;
25Salumu anali mwana wa Sauli, Mibisamu anali mwana wa Salumu ndipo Misima anali mwana wa Mibisamu.
25
26Zidzukulu za Misima zinali izi:
26Hamueli, Zakuri ndi Simei.
27Simei anali ndi ana aamuna 16 ndi ana aakazi 6, koma abale ake sanabereke ana ambiri; kotero banja lawo silinakule ngati anthu ena a ku Yuda.
28Iwo amakhala ku Beeriseba, Molada, Hazari-Suwali,
29Biliha, Ezemu, Toladi,
30Betueli, Horima, Zikilagi,
31Beti-Marikaboti, Hazari-Susimu, Beti-Biri ndi Saaraimu. Iyi inali mizinda yawo mpaka pa nthawi ya ulamuliro wa Davide.