1Phwando la buledi wopanda yisiti lotchedwa Paska litayandikira,
2akulu a ansembe ndi aphunzitsi amalamulo amafunafuna mpata woti amuphere Yesu, pakuti ankachita mantha ndi anthu.
3Kenaka Satana analowa mwa Yudasi, wotchedwa Isikarioti, mmodzi wa khumi ndi a iwiriwo.
4Ndipo Yudasi anapita kwa akulu a ansembe ndi akulu oyangʼanira Nyumba ya Mulungu ndi kukambirana nawo za mmene iye angaperekere Yesu.
5Iwo anakondwa ndipo anagwirizana zomupatsa ndalama.
6Iye anavomera, ndipo anayamba kufunafuna mpata wabwino wakuti amupereke Yesu kwa iwo pamene panalibe gulu la anthu pafupi.
7Kenaka linafika tsiku la buledi wopanda yisiti pamene mwana wankhosa wa Paska amaperekedwa nsembe.
8Yesu anatuma Petro ndi Yohane nati,
9Iwo anafunsa kuti, “Kodi mukufuna tikakonzere kuti?”
10Iye anayankha kuti,
11
12
13Iwo anapita nakapeza zinthu monga mmene Yesu anawawuzira. Tsono anakonza Paska.
14Ora litakwana, Yesu ndi ophunzira ake anakhala pa tebulo.
15Ndipo Iye anawawuza kuti,
16
17Atanyamula chikho, Iye anayamika ndipo anati,
18
19Ndipo Iye anatenga buledi, nayamika ndipo anamunyema, nagawira iwo nati,
20
21
22
23Iwo anayamba kufunsana pakati pawo kuti ndi ndani wa iwo amene akanachita ichi.
24Komanso mkangano unabuka pakati pawo kuti ndani mwa iwo amene amaganiziridwa kukhala wamkulu.
25Yesu anawawuza kuti,
26
27
28
29
30
31
32
33Koma iye anayankha kuti, “Ambuye, ndine wokonzeka kupita nanu ku ndende ndi kufa komwe.”
34Yesu anayankha kuti,
35Kenaka Yesu anawafunsa iwo kuti,
36Iye anawawuza kuti,
37
38Ophunzira anati, “Taonani Ambuye, awa malupanga awiri.”
39Yesu anapitanso monga mwa masiku onse ku Phiri la Olivi, ndipo ophunzira ake anamutsatira Iye.
40Atafika pamalopo, Iye anawawuza kuti,
41Iye anapita patsogolo pangʼono patali ngati kuponya mwala, anagwada napephera kuti,
42
43Mngelo wochokera kumwamba anafika namulimbikitsa.
44Ndipo mopsinjika mtima, anapemphera moona mtima, ndipo thukuta lake linali ngati madontho a magazi akugwera pansi.
45Iye atamaliza kupemphera, ndi kubwerera kwa ophunzira ake, anawapeza atagona atafowoka ndi chisoni.
46Iye anafunsa kuti,
47Pamene Iye ankayankhulabe, gulu la anthu linabwera, ndipo munthu wotchedwa Yudasi, mmodzi wa khumi ndi awiriwo analitsogolera. Iye anamuyandikira Yesu kuti amupsompsone.
48Koma Yesu anamufunsa kuti,
49Otsatira Yesu ataona zimene zimati zichitike, anati, “Ambuye, kodi timenyane ndi malupanga athu?”
50Ndipo mmodzi wa iwo anatema wantchito wamkulu wa ansembe, nadula khutu lake lamanja.
51Koma Yesu anayankha kuti,
52Kenaka Yesu anafunsa akulu a ansembe, akuluakulu oyangʼanira Nyumba ya Mulungu ndi akuluakulu ena amene anabwerawo kuti,
53
54Pamenepo anamugwira Iye, napita naye ndipo anamutengera ku nyumba ya mkulu wa ansembe. Petro anamutsatira patali.
55Koma pamene anasonkha moto pakati pa bwalo la milandu, anakhala onse pansi ndipo Petro anakhalanso pansi.
56Mtsikana wantchito anamuona atakhala nawo pafupi ndi moto. Iye anamuyangʼanitsitsa ndipo anati, “Munthu uyu anali ndi Yesu.”
57Koma Petro anakana nati, “Mtsikana, ine sindimudziwa ameneyu.”
58Patatha kanthawi pangʼono, wina wake anamuona ndipo anati, “Iwenso ndiwe mmodzi mwa iwo.”
59Patatha pafupifupi ora limodzi, munthu winanso anati, “Zoonadi, munthu uyu anali ndi Iye, pakuti ndi mu Galileya.”
60Petro anayankha kuti, “Munthu iwe, sindikudziwa zimene ukunena apa.” Pamene iye ankayankhula, tambala analira.
61Ambuye anachewuka namuyangʼanitsitsa Petro. Pamenepo Petro anakumbukira mawu amene Ambuye anayankhula kwa iye kuti,
62Ndipo iye anapita panja nakalira kwambiri.
63Anthu amene ankalonda Yesu anayamba kumuchita chipongwe ndi kumumenya.
64Anamumanga mʼmaso ndi kumufunsa kuti, “Tanenera! Wakumenya iwe ndi ndani?”
65Ndipo iwo anamunena zachipongwe zambiri.
66Kutacha, bungwe la akuluakulu, pamodzi ndi akulu a ansembe ndi aphunzitsi amalamulo, anakumana pamodzi, ndipo anamuyika Yesu patsogolo pawo.
67Iwo anati, “Tiwuze, ngati ndiwe Khristu.”
68
69
70Onse anafunsa kuti, “Ndiye kuti ndiwe Mwana wa Mulungu?”
71Pamenepo iwo anati, “Nanga tikufuniranjinso umboni wina? Ife tamva kuchokera pa milomo yake.”